Malaŵi
Dizko la Malawi / From Wikipedia, the free encyclopedia
Dziko la Malaŵi lomwe kale linkatchulidwa kuti Nyasaland, ndi dziko la demokilase lomwe lili ndi anthu ambiri ndipo lili cha ku m’mwera kwa Africa. Dzikoli linayandikana ndi Zambia cha ku m'madzulo, Tanzania cha ku mpoto ndi Mozambique kuzungulira kum’mawa, kum'mwera ndi ku m'madzulo. Chiyambi cha dzina loti Malawi sichidziwika bwino bwino, koma anthu ofufuza amakhulupilira kuti dzinali linachokela kwa chilankhulo cha anthu a mu dzikoli a ku chigawo cha kum'mwera, ndipo limatanthauza “malawi wa moto”, koma mbendela ya dzikoli limatanthauza "kwacha" kunena kuti dzuwa lawala m'mamawa.Purezidenti wa Malawi
Dziko la Malaŵi (Chichewa) | |||
| |||
Nyimbo ya utundu: {{{nyimbo}}} | |||
Chinenero ya ndzika | Chichewa | ||
Mzinda wa mfumu | {{{mzinda}}} | ||
Boma | {{{government}}} | ||
Chipembedzo | Protestant 55%, Catholic 20%, Muslim 20% | ||
Maonekedwe % pa madzi |
118,484 km² 20% | ||
Munthu Kuchuluka: |
{{{wamdziko}}} 153/km² | ||
Ndalama | kwacha ya Malaŵi (MAK) | ||
Zone ya nthawi | UTC +1 | ||
Tsiku ya mtundu | {{{Tsiku}}} | ||
Internet | Code | Tel. | .mw | MWI | 265 |